Vote For This Song
Lyrics
( Intro) its a love song... its ur gal Queen mishuuu its a love.. ( Verse 1) *Hello Bebie tabwela ndikuone eyaaaa *ndikakhala osakuona sindinva bwino owuwoo *chikondi chimenechi sichanormal *mkakusowa ndimafila abnormal *unapukuta misozi yangaa *pano zoliraliralira normal.. *usadzafe udzangosowa eee umandinvesa kukomaa.... (Hook) Usadzafee bae....Udzangosowaaaa Chikondi chako,,chimandinvesa kukomaaa Usadzafe bae,...unabwelesa chimwemwe mmoyo mwanga.. Usadzafe bae, love yako imandinvesa kukomaaaaa.. (Verse 2) *Am so lucky to have you..your one in a million. *Am inlove am inlove with you love yako imaposa billion.. *Ndikakhala osanvako mawu ako *Tsiku langa limabhowaa.. *Ndinathela paiwe honey usadzafe udzangosowa. *Ndikulonjeza sinzakuthawa,,,ndikulonjeza sinzakusiyaaaa.... (Hook) Usadzafee bae....Udzangosowaaaa Chikondi chako,,chimandinvesa kukomaaa Usadzafe bae,...unabwelesa chimwemwe mmoyo mwanga.. Usadzafe bae, love yako imandinvesa kukomaaaaa.. (bridge) Ooooooowa owowo owowooooo Usadzafe udzangosoooooowa Bebie Ooooooowa owowo owowooooo Usadzafe udzangosoooooowa Bebie Usadzafe udzangosoooooowaa Bebie (Hook) Usadzafee bae....Udzangosowaaaa Chikondi chako,,chimandinvesa kukomaaa Usadzafe bae,...unabwelesa chimwemwe mmoyo mwanga.. Usadzafe bae, love yako imandinvesa kukomaaaaa..×2 |
Songwriters
Queen MishuSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
9515 Plays. | 12526 Downloads.