Vote For This Song

Lyrics

INTRO AJolo Justice ( Roudeezy virus) Raj Nation Shoemaker X 3 VERSE 1 Ndabwela ndi nsapato zinayi mundipangileko zithu zinayi ndikavala zikumandigwesa phwayi sindikuzifunaso munyumba yangayi wazandimbila Foni Jolo tandipeze ndili ndi akazi folo mamuna ndekha ndangoyima ngati Polo sindikusiyanisa pagolo ndi golo ndikusoka kaye Jombo koma ndichedwelako ili ndi zilombo ndikufuna ndingoyizungulisa round chifukwa ili ndi makwacha, madollar, mapounds ndangofika angochepesa khani tagawana two, two game ili pa mpani nkazi nkuzandifusa iwe ndi Ashu kani ndat eee ndimasoka chingandivute nchani HOOK Sindine teacher..... kuwelenga sinditha ku xul sinapite sindine Dj.... kundipasa mixer ayi singamixe ndine Shoemaker ( Ashu...) shomaker. ( Ashu Ashu) ndine Shoemaker ( Ashu) Shoemaker.( Ashu Ashu) VERSE 2 tchito yanga ndiyomweyi ndiyomwe ikumandipasa mwayi bostik ndi chisongole ndizomwe zikumapezeka mu nyumba yangayi kodi mesa mumakonda Peza inu Madzi mumasamba pa guyser ndiye tingamange bwanji banja chifukwa ife uphawi unatigwila zanja iwe pano ukundika pa easy mamuna wako akumandipasa busy tchito yanga ndiyomwe ingapangise kut khaniyi mpaka ikulisise kaya mwina ndimayeselo kapena tikupanga sewelo ndiye ungavale bwanji velo pomwe ine nkalas ndimangopexa ma zelo HOOK Sindine teacher..... kuwelenga sinditha ku xul sinapite sine Dotolo zakuchipatala sindiziwapo kathu ndine Shoemaker ( Ashu...) shomaker. ( Ashu Ashu) ndine Shoemaker ( Ashu) Shoemaker.( Ashu Ashu) VERSE 3 Kodi ungandiuze zingatheke bwanji tchito yokhala yanga yanga akazi si anga ndi anu ine ndimangosoka basi!!!! Akazi ndi anu si anga ine ndimangosoka nsapato ooh nsapato ine ndimangosoka nsapatoooo HOOK Sindine teacher..... kuwelenga sinditha ku xul sinapite sindine Dj.... kundipasa mixer ayi singamixe ndine Shoemaker ( Ashu...) shomaker. ( Ashu Ashu) ndine Shoemaker ( Ashu) Shoemaker.( Ashu Ashu) HOOK Sindine teacher..... kuwelenga sinditha ku xul sinapite sindine Dj.... kundipasa mixer ayi singamixe ndine Shoemaker ( Ashu...) shomaker. ( Ashu Ashu) ndine Shoemaker ( Ashu) Shoemaker.( Ashu Ashu)

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 5623 Plays. | 2781 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram