Vote For This Song
Lyrics
[Chorus] Ukundiiwala, nde chikondi chikuwawa Chikondi chikuwawa Chikondi chikuwawa. Eh Ukundiiwala, nde mtima ukuwawa Mtima ukuwawa Mtima ukuwawa. Eh (Verse 1 , Ritaa) Kunjaku kwacha, tili pompaja Milandu yanji yosatha? Oh oh oh Unasiya kunditchula Timaina tachokondi tija Kodi waponda mwala? Zoti uli ndi mkazi pano waiwala Sumandilabadila, mwina Wapeza wina Ndayamba kukaikila, kuti udzandisiya Mtima ukuwawa Mtima ukuwawa Zikundivuta ndafuna kumvetsetsa Koma ndalephera (Chorus) Ukundiiwala nde Chikondi chikuwawa Chikondi chikuwawa Chikondi chikuwawa. Eh Ukundiiwala nde mtima ukuwawa Mtima ukuwawa Mtima ukuwawa. Eh (Verse 2, Piksy) I’ve been stressed lately, work mainly Zonse Zili bho, Chikondi still stately I appreciate that you respect me Chikondi chiyambiranso being tasty Iam sorry I let you down, Every week am out of town Babe I’m working, but thanks for checking Ndipanga zotheka kuti zonse zitheke Iam the luckiest man in the world, Ndi iwe pambalipa I can never fail Ndiwe mkazi Wakumwamba I can tell, Nde usamadandaule you’re my girl. (Chorus) Ukundiiwala nde, Chikondi chikuwawa Chikondi chikuwawa Chikondi chikuwawa. Eh Ukundiiwala nde, mtima ukuwawa Mtima ukuwawa, mtima ukuwawa. Eh Ndili ndi mantha, ndingadzagende Katauluka. Oh no, oh no... Ndiwe wekha, sukubetsa Umabebetsa sakugwetsa Akulenga, sakuvencha Ndine chips, iwe ndiiwe Ketchup (Chorus) |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
