Vote For This Song
Lyrics
Give thanks for the life, almighty God Jah/ Listen Mtima wanga sukumvesa/ msonzi yokha ikungogwa Maso anga atopa sakuona Chisoni change ndi fuko langa/ dzukani osagona Mtundu kutha inu mukuona Oposa sazindikira/ anzeru adanka kuti Miyambo yachikuda/ kutengera zitisambula Pakuti ife/ oah oah eih eyah Chorus Tisiyana Chikhalidwe/ tisiyana kochokeraTisiyana Chikhalidwe/ tisiyana kochokera Chete wanga sikupusa/ musandiwete ngati galu I got the right to say whats on my mind Ndinu nomwe mwachita izi/ ngakhale mwana akudziwa Nanga inu osangovomera Mukulemekeza alendo/ kuwapasa chuma ndi malo Eni nthaka/ kwao ndi kupemphapempha basi Katangale ndi ziphuphu/ kusakhulupirika udindo Eni nthaka/ kupwetekana tokhatokha basi Chorus Tisiyana Chikhalidwe/ tisiyana kochokera Tisiyana Chikhalidwe/ tisiyana kochokera |
Songwriters
Prince Martin, Joel Suzi aka Suzi Marcus and Rahim Ibrahim aka Ghetto ProphetSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Chikhalidwe is taken from Reggae Revolution the second album from the Soul Raiders
Comments

Reggae Revolution Songs | Ndayima Pa Nsanja » |