Vote For This Song
Lyrics
Intro: We here Ine eeh, ah ah Ine eeh, ah ah Maluzi ziii, (musiye mzako) ah ah Maluzi ziii, (musiye mzako) ah ah Verse one: (Saint) Munthu wandalama kuitana okukonda ambiri Mpaka dollar akudyere kenako akuipitsire mbiri Nde maluzi akapweteka Amzako onse chekacheka Abaleso sapezeka Pakamwa pawo adacheteka Ukatha ma plan Ngati udye makatani Maluzi ndi chipani Choyambitsa udani Ineee. Chorus: Aah Ine ine yah Ndatchekela Maluzi ndalephela (ah) Aah ine ine yah Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah) Ndangosanduka wolira Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah) Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah) Ndangosanduka okanda Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah) Eeh ndalephela Vers 2 (Macelba) We here Kuyesesa kusaka ndalama Titole chikwama titule minyama Kuyesesa kuthesa ulova poti zikamavuta palibe akutchova Kuthamangathamanga daily Koma mavuto angochuluka daily Mpaka pa line angondikamba Ndichite bwanji kuti ndipeze mpamba Wangongole afuna zake Mkazi wapakira zake ati apita kwa make Mwina ndiyese mtera kapena ndilowe kuba Kukhesa thukuta koma maluzi sakumva ine BACK TO CHORUS Bridge: (Macelba) Musiye mzako ×8 (Saint) mmmh ine eh eh Maluzi ah ah Ine.. mayo mayo. BACK TO CHORUS. Outro (Saint) Ndalephela, ndalephela aaah ah ah ×4 |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
