Vote For This Song
Lyrics
Intro Yoh x9School ndinamaliza Yoh X9 high grade yoh Verse 1 Chillin pon di corner wit my buddiesZomwe timapanga sitiwopa police Smokin high grade all day ntchito tilibe pano kuno anthu tinatha ma plan Yeh ndayesa kugulisa mpunga Ndayesa kuyimba komabe osatchuka Ndayesa kugulisa msomba kugulisa thobwa kuthamanga mpakana mpamba kudukaa (Eeeeeeeh) Kodi ndani anandilodza ine Please chonde muwuzane ngat mulipo chonde muchenjezane ine ndat (Eeeeeee) Kodi ndani anandiloza ine now I can't walk,I can't talk, I can't jog till I smoke HOOK School ndinamaliza (Eeeeeeee)Koma ntchito sikupezekaaa (Eeeeeeh) Zibwenzi sizikuyendaa,nazo ndlama kusowa ngat tinayambana So I smoke some high grade (Alright) Smoke some high grade (Alright) Smoke some high grade (Alright) Smoke some high grade (shaaaa) Smoke some high grade (Alright) Smoke some high grade (Alright) Smoke some high grade kut ma stress achokee Verse 2 School fees ikusowaOkoma mtima nawo akusowa Chamba chokha ndi chimene chikupezeka Chikasowa ndekut upezeka ndi mowa Ndlama nazo zikusowa Banja nalo likusowa Chochita nacho chikusowa Ikakhala mphasha nayo ikusowaa ndayesa kugulisa mpunga Ndayesa kuyimba komabe osatchuka Ndayesa kugulisa msomba kugulisa thobwa kuthamanga mpakana mpamba kudukaa (Eeeeeeeh) Kodi ndani anandilodza ine Please chonde muwuzane ngat mulipo chonde muchenjezane ine ndat (Eeeeeee) Kodi ndani anandiloza ine now I can't walk,I can't talk, I can't jog till I smoke. HOOK Outro AlrightX8 yoh haha Stich Fray on thisEeeh high gradeX3 AlrightX8 |
Songwriters
Stich FraySharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
High Grade is a heavy and banging dancehall tune cementing Stich Fray's status as a top contender for the dancehall crown on the Malawian dancehall scene. Download and enjoy!
Comments
