Vote For This Song
Lyrics
Hook Lero kalikiliki/ Lero lokha kuli kalikiliki/ Lero kalikiliki/ Lero tigona koma pankitikiti/x2 Verse 1 Wantali likiliki Wamfupi likiliki Oonda likiliki Onenepa likiliki Lero tikoka ma chick chick Ndati tikoka ma pretty pretty Bawa iliko zikwizikwi Dance yake sick sick Fans kutenga ma pic pic Bwera titenge chi pic pic Ndingobwera mwa peace peace Simafana ama kick kick Palibe zomavaya pretty Mpakana titathana psiti Itanako anzako 50 Ndabwera ndi mamemba 60 Hook Lero kalikiliki/ Lero lokha kuli kalikiliki/ Lero kalikiliki/ Lero tigona koma pankitikiti/x2 Verse 2 Wantali pokopoko Wamfupi pokopoko Oonda pokopoko Onenepa pokopoko Town yonse pokopoko Line yonse pokopoko Phazi liri dokhodokho Vina ngati bokhobokho Atagone zakezake Aliyense wakewake Ndati yense chakechake Palibe andisakesake Wamng'ono sangamake Akayamwe kwa make Tulo lero lindilake Wina mpaka italakwe Hook Lero kalikiliki/ Lero lokha kuli kalikiliki/ Lero kalikiliki/ Lero tigona koma pankitikiti/x2 |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
