Watch and Download Music Video



Download this video

Vote For This Song

Lyrics

So lonely,am so lonely,so lonely. Verse 1 Munayesetsa kudamager simapeza nazo tulo Pakamwa panupo ndati zitopotopo kusowa nazo mpumulo Kwanthawi yaitali mwasokoneza banja langa Zonyoza zambiri zomangofuna akazi anga andisiye ine ndekha ndekha ine ndiri padzuwa ine ndikungolira ine mpaka… Chorus Aaah… apita akazi anga Aaah…ayenda adona anga*4 Inu chimwemwe kutsayako Verse 2 Jus tell me watch want moyo wanga Poyamba mudandidanitsa ndimakolo anga Kenako kundidanitsaso ndiabale anga Ndizanga zonse chifukwa cha inu Why oh why Nkhani yakunyumbayi kwanga,imathera pa facebook Why oh why.. Nkhani yam’banja mwanga,imathera pa whatsapp group Pamtondo ndipo zimathera nkhani Zabanja bwanji zikukukhudzani Ehh,,,Kodi nalakwitsa kukudziwani mkaziyo mutenge ndinu tchukani Chorus Bridge. Am so lonely,*3 Ndekha ndekha Am so lonely*4. Chorus

Songwriters

Saint, Red Disk Records

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 60808 Plays. | 93731 Downloads.
Akazanga Songs Akazanga [Reggae Version] (Prod By OBK) »

Follow Malawi Music on Instagram