Vote For This Song
Lyrics
Verse 1: Timano tako ukamasekelera Timau tako ukamandiyandkhula Timaso tako ukandiyang'ana,, ndimafa head Timiyendo tako ukaponya step Kambina kako mkumagwedezera Timanja tako tikandikhudza ndimadzifunsa aah.. kuti,,, Pre chorus; Sudzandidyera chuma changa iwe Delilah Sudzawazunza abale anga iwe Delilah Mkundipereka kwa adani Ngati Delilah..*2 Chorus;; Delilah ah ah aaah Unene eeh eh Delilah ah ah aaah Unene eh eh Delilah eeh eh Unene eh eh Ndidziwe Delilah *2 Verse 2 Mwina umphawi wanga siudzatha chifukwa cha iwe Abale ndi amzanga mkudzadana chifukwa cha iwe Mwina udzandiika pampeni, kwa adani anga nena zeni zeni Iwe, siwe woyendayenda ngati enawa/ Sudzanditengera matenda mkundithawa ine Ndimapemphera// kodi mkubwera kwako simdzasochera ine? Mbuye adandidalitsa kodi mkubwera kwako sanditembelera ine? ndidziwe, kapena mwina ntchito mkudzatha Kapena mwina mdzayamba ine kupita... kumanda mtakusiya ndi ana, unene kodi udzawasamala. BACK TO THE PRE CHORUS BACK TO THE MAIN CHORUS Bridge ;; Delilah ah, simfuna kudzalira aah Ngati Samson,ngati samson I say Delilah Sindikukaikila aaah koma ngati samson, simfuna kudzalira aaaah |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
