Vote For This Song
Lyrics
NYAU LYRICS Verse 1 (Snag Bomaye) Zalowa zayala nkhutumu kamphasa/ Nabola tadzala mmutumu zidzapsa/ Chimodzi ndimantha, ziwiri mapasa/ Limodzi ndi phata ambiri tatasa/ Mkati mwa bibida zilungamo zadzadza/ Ndi nthawi chabe ah zitisambwadza/ Osautsanza, mtima suvala nsaza/ Tatola zobweretsa bata ndigwire chanza/ Nduvomereza kudikira ndzikhomo/ But u don't need to rush, chitseguka chikhomo/ Dzulo Lavaya leroli ndi dzisomo/ Awawa awowo akudutsa momwemo/ Lunga lunga nkubadwa ndi mau/ Zosekaseka zopusa za ziii mihawu/ Muona nkhanga mipala mashawu/ Ndunena afana obizika kundisemela nyau/ Chorus (Bwabz) Awa si anzathu/ Tawatulikira, moto tikayatsa iwo amatidzimitsira/ (Nuff ah dem nah real) Zinyawu amatitsemera/ Ngini zathu iwo amakhomelera/ Tawatulikira, moto tikayatsa iwo amatidzimitsira/ (Nuff ah dem nah real) Zinyawu amatitsemera/ Ngini zathu iwo amakhomelera/ Verse 2 (Eagleeye) I'm still going to rap like nobody's business/ Khon'uba iRap ayindibhatali ungena phi? That's none of your business/ Bohluleka kwi foundation bethela manzi/ ndisokha Not knowing very well ukuba ndim ababemokha/ Ngob'ezingoma ziyokha/ Nibaxelele naba babendi mocker/ Namhlanje ndiya elevate i talk ndiyayi walker/(ha ha) I started this ndiseyi mveku/ Blessings on the way Ndicela zindithandazeli nceku/ Ndikwazi ubamandla ndingalahli tawuli okwexelegu/ Ndingaze ndi lose patient Ndibe namandla wesihelegu/ Kudala ndagqejw'iNgongoma/ As ba ndikhula ndaqaphela ibingekaqal'INdaba ibiseziNgongoma/ I'm a fan of myself xandi feel pressure kweziye artists ezenzi game ibe shushu I cool my self down/ ndiyazipholisa I will never step down/ To reach my goals I never play foul/ Chorus (Bwabz) Awa si anzathu/ Tawatulikira, moto tikayatsa iwo amatidzimitsira/ (Nuff ah dem nah real) Zinyawu amatitsemera/ Ngini zathu iwo amakhomelera/ Tawatulikira, moto tikayatsa iwo amatidzimitsira/ (Nuff ah dem nah real) Zinyawu amatitsemera/ Ngini zathu iwo amakhomelera/ |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
