Vote For This Song

Lyrics

INTRO Its your boy Singlay VERSE 1 Chimwemwe changa nthawizina chimadzabwelera m'mbuyo Makamaka ndikakumbukira nthawi yomwe takhala limodzi Ndithudi sindinkaganizira kuti ungadzachoke chonchi koma chinachake chimandiuza kuti uli ku paradizo (paradizo) CHORUS Ngakhale ndikudziwa uli pabwino koma ndakusowa-ah Ngakhale ndikudziwa uli pabwino koma ndakusowa Iwe ndakusooowa ndakusowa-ah x2 oh noh VERSE 2 Ndikamakhala nthawizina ndimangokhetsa misonzi makamaka ndikakumbukiraaah zoti iweyo unapita Kungochoka osatitsanzika? Kodi kukhala amatero? Chonchobe poti ndi chikonzero cha mwiniwake Mulungu CHORUS Ngakhale ndikudziwa uli pabwino koma ndakusowa-ah Ngakhale ndikudziwa uli pabwino koma ndakusowa oooh BRIDGE Ndikuyenera kudziphunzitsa kumwetulira nkamayang'ana chithunzi chako poti padzikolino palibe wamuyayaaaaaaaah! Ndikuyenera kusiya kulira poti chiyembekezo chilipo oh kuti tsikulina tidzaonanaah CHORUS Iwe ndakusowa x4 Ndakusowa x2 Oh noh x 5

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 14876 Plays. | 9455 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram