Vote For This Song
Lyrics
Verse 1 ngati ulibe skinny jeans iwenso nde kaya ngati umabwela ku den basi kazivaya sindinyengelela bebi ine ndi one wire pokha pokha ngati mwina umayimba choir yemwe alibe skinny jeans ndi mkazi wa chimidzi fungo lake mkamwa kukhala ngati la chiphwisi zija zodya mpunga pa nthawi ya khirismis kamwa langa si sunga zinthu za chisinsi umandipeza poti si uvala za make dzana makamaka zija zomwe unavala dzana ndikukakamila mpaka ndikupase mwana buluzi wa pa easy, chiseko china m'mpana ur my range lover every time you bend over r u ready 2 tell ur boy "the game over"? awa si masamu sizofunika ku sova ndiku gogodela ngati a mboni za yehova Chorus Umandipeza ukathinisa ndi skinny jeans uzalola ndizakufusila by any means ndi ka skinny jeans * 2 Umandiwaza ukathinisa ndi skinny jeans uzalola ndizakufusila by any means ndi ka skinny jeans * 2 Verse 2 skinny jeans make me look like bad like bad spencer yandi pangisa ku gwila bebi ku deni ya a neba usiku ose osagona june bad weather magesi akangoti azima, time 2 go further shes malawian but looking like american the way she dresses cool nanga these ladies can ka kiss kake ndi kokoma ngati sugar cane kandi pangitsa kusamba madzi amu water can my sweet sixteen skin' jeans size fifteen zilibe kanthu wether ur too fat or too skinn' ukangodutsa fanzi imayamba sweating usiko wonse baby tikhalila texting u be the mother of my kids, i'll be the daddy chimakoma chilichonse ungaphike kuvala kwake ngati ulendo waku party mu skinny jeans pa 1 mpaka pa sate Chorus Umandipeza ukathinisa ndi skinny jeans uzalola ndizakufusila by any means ndi ka skinny jeans * 2 Umandiwaza ukathinisa ndi skinny jeans uzalola ndizakufusila by any means ndi ka skinny jeans * 2 Verse 3 Nkhani ili nkamwa pano ndi ya skinny jeans akangoti wasamba samba ndimu skinny jeans ka mini skirt katha fasho koma skinny jeans skinny thong, skinny short, everything skinny skinny jeans paliponse ngati hule spana ka house girl koma so ti ana ta mabwana too late ukamazaziwa uta pana umazitenga ngati dolo iwe umanama mu skinny jeans pa stereo nkhani sawasawa ma bebi wa usayese abwelela bawa amafuna wodula komasa osawawa iwe kungo gula umodzi kenako kuthawa phazi thandizeko awa tiwonana mawa amabwela okha ngati madzi ku chikwawa alibe ulemo, amadutsa olo kuti wawa nkhani ya ma bebi pa malawi ndi kawawa Chorus Umandipeza ukathinisa ndi skinny jeans uzalola ndizakufusila by any means ndi ka skinny jeans * 2 Umandiwaza ukathinisa ndi skinny jeans uzalola ndizakufusila by any means ndi ka skinny jeans * 2
|
Songwriters
Tweeza, The DareDevilsSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
