Watch and Download Music Video



Download this video

Vote For This Song

Lyrics

Tidziwe Multiplication Tiyeni tonse, tidziwe multi, multiplication ×1 (by Tanaka) Tiyeni tonse tiroweze multiplication table, tiroweze multiplication table Double! ×2 (by Tanaka & STD4 learners) Multiplication ingakukankhireni kwakuya Maso pa tsogolo, maso pa tsogolo Munga pange zazikuru, yeah Triple! ×3 (By STD8 learner) Rap part Ndakana ulesi Ati ndi sukulu sizigwirizana mmesa Nde pofuna kulemba masamu Kuwonera kuchikuto daily Kapena ndingo kopera after Mary? Kukanika kuloweza multiplication table? From the beginning to the end of the term Yesera mbaliyako the teacher is not to blame Pena zimavuta eeh! Pull up your sock eyes on school school! Zomasolver solvers ndani adayambitsa? Adalimbitsa moyo pena zimandi dwalitsa Eh ndipatse calculator Vuto ndipamayeso adzandi landa a invigilator Bola ndingo loweza kanyimboka basi Ndikapempha ku Domasi kakhale msilabasi, yeah ×4 (by Hamjee) Multiplication ndimaziko a masamu, yeah Nambala yayiliyonse 0 kapena 5! ×5 (VIC) ×6 (by Hamjee & Lucia) Multi, multiplication Osa gonja! ×7 (by Yui) ×8 (by Yu) Ngati muroweza multiplication, muthakuphunzitsa ena, kulimbikitsa ena ×9 (by Yui & Yu & STD4 learners) Ok, ×10 (by VIC) Tiroweze, tiroweze, ka nyimbo ka tiroweze ×11 (by Yui) ×12 (by Yu) Tiroweze multiplication table, kunyumba kusukulu kulikonse, kulikonse, kulikonse, kulikonse Tiyeni tonse, tidziwe multiplication

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 9935 Plays. | 2772 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram