Vote For This Song
Lyrics
STICH FRAY Anthu ambiri amakuseka Ndidziwa mtima wako umapweteka Anthu akwanu amakunena Ndidziwa azimzako ambiri amakunyoza iwe Zambiri umazimva, zoona umazimvazo Koma ndine munthu am not perfect ndimalakwaso Mbiri yanga angayidese bwanji u'll always be my baby Well listeni mi nah care wah dem seh coz am down for you baby. Chorus..... Ngat simunayimvele kayipezeni pa Malawi music ilimbweeeee guyz... |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
