Vote For This Song
Lyrics
YOSHUA ALIKUTI CHICHEWA LYRICS Verse Ana a mulungu Aisiraeli azunzika m'chipululu Bambo Mose musatayilire Namalenga ati mulamulire Lero mwataya chipangano Kuyamba kupembedza makavalo Chorus Alikuti yoswayo Adzabwera liti Tifuna chipulumutso Bridge Wanyoza mtundu wanga Iwe walakwa x2 Waphetsa mtundu wanga Ndati walakwa x2 Back to chorus Alikuti yosuayo Adzabwera liti Tifuna chipulumutso Sitifuna mose wina Wankhambakamwa Wodzatisocheretsa
Second verse Ulendo wochokera kwa iguputo Unali wautali Munatiwolotsa yolodani bwinobwino Nanga lero bwanji Kabwino konse upange ulalike utakwera chulu Namalenga sakondwa nazo Mphoto yako Udzalandiliratu
Bridge
Chorus |
Songwriters
The Very BestSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Yoshua Alikuti by The Very Best.
Comments
15358 Plays. | 3044 Downloads.
« Kondaine ft Seye | MTMTMK Songs | Come Alive ft Mo Laudi » |