Vote For This Song
Lyrics
Verse 1 Baby Mtima wanga unautenga Ndipo mzimu wanga unavomera Ndisaname unkandipatsachimwemwe eh There was only you, ndimapanga za iwe Mami Mami unandiswera Mtima wanga Mami mami utandibera Mtima wanga I was convinced kuti ndapeza Mtima wanga wadekha. Hook Nkhani ya chikondi? Imandigwetsa nsonzi Kapena mwina ndi ngozi? Unandisiya chonchi? Unandisiya Misonzi x4 Verse 2 Mesa unkandikonda? Ine ndinkakukonda baby Ife tinkakondana , atleast that's what I thought Oh baby How did we end up here eh? Olo unandisaya bae ,Ndinkakukonda x2 Panopa nkhani ya chikondi? Imandigwetsa nsonzi Kapena mwina ndi ngozi? Unandisiya chonchi? Unandisiya Misonzi x4 Bridge Unandisya Misonzi x 8 Hook Nkhani ya chikondi? Imandigwetsa nsonzi Kapena mwina ndi ngozi? Unandisiya chonchi? Unandisiya Misonzi x4 |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
