Vote For This Song
Lyrics
Verse 1 Anzanga a age anga pano anakwatira// anapeleka phaa nkazi anawanyanyalira// anasiya geri nkuyamba ma gobo// wez penda penda pano zikuyenda bhobho.. Anzanga ah age yanga ena Ali pa vep// ife tikadali jobless koma sitiluza faith// mwayi ulipobe ngat sinatipeze death// Timangopempha jah jah ationjezele strength.. Anzanga Ena kugeri sanali magenius// Koma pano anaiphula akuyendera ma hirux// omwe tinkakhozafe umphawi watiyanja // Timagulitsa Zibwente kuti tidyese banja.. ah life ndichoncho//Pena zimayenda pena kugwera kumphopho// uzasutha one day sungangokhala pompo// osapanga phuma zizayera opanda sopo// Verse 2 Ungokhala ngat tsokonombweee// utha ntunda nkudupha ndukuuza tsokonombwe/ umafuna kuphura mwachangu ulowa nazo umbanda// yesa mahaso angapo sachezelera nyimbo imodz mganda.. Mulungu anakupasani.chuma kuti muthandize opelewedwa// malo motithandiza mpameneso tikubeledwa// Mdaliso wa mulungu mwasandusa chotilangira// ndife atsokonombwe pano one day muzatigwadira Osaiwala Kuthamanga sikufika malume// njalezo ndizanu koma chuma ndi mbalume// tizapaka chitosi pomwe muzatilume// mano azavunda simuzadya nao beef yothira wa mame.. Koma...aah life ndichoncho//Pena zimayenda pena kugwera kumphopho// uzasutha one day sungangokhala pompo// osapanga phuma zizayera opanda sopo. |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
