Verse 1
Maso ako atumizah uthenga ku thupi lako lonse ati zomwe aona
iwo oh oh zokhumudwitsa makutu ako aukila thupi lako lonselo ati
zomwe akunva iwo oh oh nzosangalatsa (maso awona) kunyasa kwa
nsapato yanga nanji ndi ntchito yanga ya manja yopanda swagga wafooka
poti anzako adapeza wa suit pa watsapp adaika zithunzi
Hook
Nsabise mamie mwandisangalatsa
Mwapeza malo mundimwanga kodi ngachite mwai okhala mudziko lanu kapena
mwina..........
Chorus
Ine nkadzavula (ovololoyi)
Nkadzavula. (Ovololoyi)
Mwina udzakhala wanga x2
Verse 2
Mwina nkumadabwa ndalimba ntima bwanji ukadzaona fumbi gilizi kumanso
kwanga nkumadzifunsa walakwanji poti ntchito yanga nkachidutswa
pamaso pako
Rich mind poor body Mamie I swear
All I want is the beauty that your smile gives
You’re all I want
All I want yeah
You’re all I want
All I want
All I want is you
Hook
Nsabise mamie mwandisangalatsa
Mwapeza malo mundimwanga kodi ngachite mwai okhala mudziko lanu kapena
mwina..........
Chorus
Ine nkadzavula (ovololoyi)
Nkadzavula. (Ovololoyi)
Mwina udzakhala wanga x2
Bridge
Ntchito yanga njonyasa
Zovala zanga ndi nsanza
Koma tsogolo langa ndilowala
Nzeru zanga nzosiyana