FULL NAME: Isaac Manda
GOSPEL ARTIST, Known as MANDAHA
BORN: 1992
TRIBE: Tonga
HOME VILLAGE: Nkhata-Bay
CURRENT RESIDENCE: Mzuzu
MARITAL STATUS: Single
Education background, form Four
Am also holding a Certificate in HOTEL AND CATERING MANAGEMENT.
MY FAVORITE BREAKFAST: Smashed Avo on toast with same fried Eggs, Bacon and hollandaise sauce on top. and English Breakfast.
WITH SAME
. Hot chocolate
. Rooibos tea
. Chai latte
MY FAVORITE FOODS:
Hake Fish, Snoek Fish, Salmon Fish, Mushroom Risotto, Chicken Pasta and KFC.
MY FAVORITE DRINKS:
. Banana smoothies
. Iced Coffee
. Rock shandy
Locally EMBE JUICE.
MY FAVORITE LOCAL ARTIST: Skeffa Chimoto
MY FAVORITE INTERNATIONAL ARTIST: Don Moen
I started ministering when i was young, ndayimbapo ma choir muma church osiyana osiyana omwe ndakhara ndikupemphera kuchoka umwana wanga.
Kuyimba pandekha ndinayamba 2016, chomwe chinachitika ndi choti ndinatalikirana nawo ma choir onse omwe ndinkayimba nawo nde komwe ndinaliko ndinkamva kupelewera pa moyo wanga, and i started praying for it kuti Mulungu andiwonetsera chomwe iyeyo akufuna kuti ndikhare. Nditatenga nthawi kupempherela chinthu chija ndipomwe ndinamva mawu oti ndayenera kuyamba kutumikira kudzera mumayimbidwe. That's how i started my Music Ministry.
Pakali pano ndili nyimbo more than twenty, koma zomwe anthu akhara akumvelapo muma Radio stations ndi monga: CHIKONDI, MUSANDISIYE, CHISOMO, ZGOLO NI YESU, MWENEKU MBUYA, ONDISAMALA, LAPA, NDAKONZEKA, WALANI YESU komanso DZINA LANU.
Sindina tulutsepo ALBUM chiyambireni chifukwa cha mavuto azachuma omwe ndakhara ndiku kumana nawo, koma ma Album omwe ali ready as of now ndi awiri, oti ndikapedza ka ndalama ndikhara ndikuwa tulutsa kuti anthu akhare akudalitsika ndi utuliki wanga.