Vote For This Song

Lyrics

verse 1 ndikakhala zimandivetsa chisoni/ ndenkha manyazi amandipeza kuti ndikupatse moni/ poti ndine munthu oipa kwambiri/ poti unafunitsitsa kuti tizakhale awiri/ ndine amene anawina mtima wako/ poti ndine amene umanyada naye kwa anzako/ umati uli ndine wapamtima pako/ koma ndine amene makusewera chipako/ panali ambili amakufuna koma umati uli ndine/ za akwanu sumava zoti tisiyane iwe ndine/ ndinachongetsa aliyese amaziwa/ unalinane pali pose zachibwana umapewa/ koma ndine olakwitsa kwabasi/ ndimakonda akazi/ ndinakuswera mtima/ you didn't believe it utandipeza ndi wina/ kupepesa ndikwanga, munthu amalakwitsa imva mau anga/ ngakhale bho sunayankha, unasithilatu mawanga/ tipange chimodzi/ pano madzi ali nkhosi/ tizakhale limodzi/ iwe ndine pamodzi/ chorus ndine ndinayambitsa ndine/ ndinakuswera mtima/ zinthu zako zinaima/ koma chomwe ndikupepha ine ndi mwai wina/ poti zosezi ndine/ ndinalakwitsa ndine/ ndikupepesa ndine ndine ×2 tibwelerane iwe ndine verse 2 pano umati sungakonde mamuna/ unalumidwa ndi chakuda/ koma chomwe ndikupepha ndi mwai wina/ ngakhale pano umandida/ when am texting you umachulutsa ma delays/ koma ndine to make you kundipewa nowadays/ undipangitsa ndidwale/ koma zakale uiwale/ mpaka kale tizakhale/ ana tizabale/ tizathandize achibale/ tsogolo lanthu lizawale/ ndikudikila yankho lako/ dziwa ndine nthiti yako/ bambo wa ana ako/ ndikufuna kukhululuka kwako/ unalinane palipose kulikose limodzi/ mkakumbuka zanthu zose chilichose pamodzi/ am begging you ndipatse mwai wina/ tizapange zina/ tizakhale limodzi/ iwe ndine pamodzi/ no one plans to make a mistake/ but it's a mistake to repeat a mistake/ chorus

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 6029 Plays. | 1797 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram