Vote For This Song
Lyrics
Mdyelekezi M ngotuzuka M ngotuzuka mngotutuzuka, mdyelekezi M ngotuzuka atuzuzuka kwambiri akawona ine!!!! mdyelekezi atuzuka kaona Ine ,alekelenji utuzuka kaona Ine?akamagenda mumtengo muli kanthu.chifukwa chake atuzuka akawona ine*2 Koma mbuye walonjeza kumenyera nkhondo Ine ngati mordecai pamaso pa Harman yo!mlungu wanga walonjeza kumenyera nkhondo Ine ngati David pamaso pa goliaght yeah. chorus mdyelekezi M ngotuzuka M ngotuzuka M ngotuzuka. mdyelekezi M ngotuzuka atuzuka kwambiri akawona ine!! amandiona ndili ndi yes ineyo,amanditutumuka mchifukwa chake atuzuzuka akawona ine. verse 2 adani anga atuzuka akawona ine, alekelenji utuzuka akawona ine?akamaloza mumtengo muli kanthu mchifukwa chake andiloza akawona ine*2 Koma mbuye walonjeza kumenyera nkhondo ine ngati yehosofati pamaso pa a amon wool! mbuye wanga walonjeza kumenyera nkhondo ine ngati ayisilayeli pamaso pa iguputo M mmm back to chorus. verse 3 adani Ako atuzuka akawona,alekelenji utuzuka akawona iwe?akamagenda mumtengo muli kanthu mchifukwa chake atuzuzuka akawona iwe*2 Koma mbuye akulonjeza adzakumenyera nkhondo ngati Daniel mumdzenje lamikango.mbuye wako akulonjeza adzakumenyera nkhondo ngati achina misheck mung'anjo yamotoyo!! chorus fading |
Songwriters
Born Kavala BandaSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
18628 Plays. | 7089 Downloads.