Vote For This Song
Lyrics
Intro Mmmm Mr ayaya Ndakupatsa zanga zonse Undisamalire mmmm Undichengetere eeh VERSE 1 Taonani hunie komwe ifeo tachoka / Analipo ambiri sankadziwa lero tizafika / Bae you my sunshine / I see the future / Ndiwe moyo wanga basi “Basi!!!” / Tenga zanga zonse basi “Basi!!!” / Sindifuna kulira kusweka mtima ndinadutsamo / Sindifuna kukhala ngati makoko amango / Kunditaya palipose / Kundisiya palipose / Wina azachileka / Wina azandisimba / HOOK Ukazandisiya / Opanda notice ngati nyumba ya rent / ……[kaya!!!]…. Summon kundidulira / Kulikonse kundipitira / Sindizayimva / Ndizapita ku court kukatenga objection / Sindizalora / Ndizapita ku court kukatenga objection / Pazamfa zungu pano / “mbambadi!!” Pazatelera ndati / “mbambadi!!” Ine ndizapita ku court kukatenga objection / VERSE 2 You promise to be the best person / Am gonna be now good enough / Ndapeleka nkhoza la mkuwa / Likhale chikole / Chikondi chokoma ngati ichi ndi machisowa / Usakhale aja / Anandipaka-paka matope / Kunditaya palipose / Kundisiya palipose / Wina azachileka / Wina azandisimba /HOOK Ukazandisiya / Opanda notice ngati nyumba ya rent / ……[kaya!!!]…. Summon kundidulira / Kulikonse kundipitira / Sindizayimva / Ndizapita ku court kukatenga objection / Sindizalora / Ndizapita ku court kukatenga objection / HOOK Ukazandisiya / Opanda notice ngati nyumba ya rent / ……[kaya!!!]…. Summon kundidulira / Kulikonse kundipitira / Sindizayimva / Ndizapita ku court kukatenga objection / Sindizalora / Ndizapita ku court kukatenga objection / Pazamfa zungu pano / “mbambadi!!” Pazatelera ndati / “mbambadi!!” Ine ndizapita ku court kukatenga objection / |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
650 Plays. | 392 Downloads.