Vote For This Song
Lyrics
*Intro* Sin'nadziwe...(x2 *_Taurai..._* *Verse 1* Ankatonena'wo Malaya ndi amodzi iwe Ankatokamba'wo Kabudula zigamba tho! Ati sitepe yako Pobwera ngati ukupita Ankakutcha _pewani_ iwe Ankati 'Love is Blind' Pa iweyo ndinabetsa eeh Ankayesa nditekeseka ine Ona lero mitu angopukusa aah Sakumvetsa... Lero ankhoswe nkhuku akhadzulirana *Chorus* Sindinadziwe eyaye kuti kukhala kuli choncho. (Sindinadziwe eyaye kuti kukhala kuli choncho). Kundinyozera mamuna inuyo Ine zimenezo nde toto... Ndakonda yemweyu ineyo Yemwe azandisunge. *Verse 2* Akanadziwa sakananeena You're my everything My honey'wo My sugar sugar (x2) M'maluzi tikhala imodzi (Limodzi...) M'mawini tikhala limodzi (Limodzi...) Coz you're my everything My honey'wo My sugar sugar yeeee-yeeeh *Chorus* Sindinadziwe eyaye Kuti kukhala kuli choncho (Sindinadziwe eyaye Kuti kukhala kuli choncho) Kundinyozera mamuna inuyo Ine zimenezo nde toto (Ndakonda emweyu ineyo Yemwe azandisunge) *Bridge* Ankatonena'wo Malaya ndi amodzi iwe Akanadziwa Sakananeena Akanadziwa Sakananeena You're my everything My honey'wo My sugar sugar M'mawini tikhala limodzi (Aaayeeee) M'maluzi tikhala limodzi (Aayeee) Coz you're my everything My honey'wo My sugar sugar heeh!!!! Iyeee Ooooh *Chorus* Sindinadziwe eyaye Kuti kukhala kuli choncho (Sindinadziwe eyaye Kuti kukhala kuli choncho) Kundinyozera mamuna inuyo Ine zimenezo nde toto (Ndakonda yemweyu ineyo Yemwe adzandisunge) (x2) Ng'yakuthanda wena Ng'yakuthanda mina Eee umuntu wami. |
Songwriters
TauraiSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
In the song, Taurai sings about a lady who has finally happily got married to her sincerely boyfriend despite insults from family, friends and relatives who were discrediting the man because he is poorComments
